2 Kings 10:22 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsono Yehu adauza munthu wosunga zovala kuti, “Bwera ndi zovala zopatulika zokwanira anthu onse opembedza Baala.” Munthuyo adaŵatengera zovalazo anthu aja.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Nati kwa iye wosunga nyumba ya zovala, Tulutsira otumikira Baala onse zovala. Nawatulutsira zovala.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndipo Yehu anawuza munthu wosunga mikanjo kuti, “Bweretsa mikanjo yokwanira atumiki onse a Baala.” Ndipo iye anabweretsa mikanjoyo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Nati kwa iye wosunga nyumba ya zobvala, Turutsira otumikira Baala onse zobvala. Nawaturutsira zobvala.