2 Kings 10:26 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndipo adatulutsamo chipilala chopatulika chimene chinali m'nyumba ya Baala nakachitentha.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Natulutsa zoimiritsa zija zinali m'nyumba ya Baala, nazitentha.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iwo anakatulutsa mwala wopatulika umene unali mʼnyumba ya Baala ndipo anawutentha.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Naturutsa zoimiritsa zija zinali m'nyumba ya Baala, nazitentha.