2 Kings 10:27 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Motero asilikaliwo adaononga chipilala chopatulika cha Baala, naononganso nyumba yake, ndipo adaisandutsa chimbudzi mpaka lero lino.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Nagamula fano la Baala, nagamula nyumba ya Baala, naiyesa dzala mpaka lero lino.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Anawononga mwala wopatulika wa Baala ndi kugwetsa nyumba ya Baala, ndipo anthu anayisandutsa chimbudzi mpaka lero lino.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Nagamula fane la Baala, nagamula nyumba ya Baala, naiyesa dzala mpaka lero lino.