2 Kings 10:3 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
mwa zidzukulu za mbuyanu musankhule mmodzi wooneka bwino kwambiri ndipo mumloŵetse ufumu wa bambo wake. Kenaka mukonzekere nkhondo kumenyera banja la mbuyanu.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
musankhe wokoma ndi woyenerayo wa ana a mbuye wanu, ndi kumuika pa mpando wachifumu wa atate wake; ndipo muiponyere nkhondo nyumba ya mbuye wanu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
sankhani mwana wa mbuye wanu amene ndi wooneka bwino ndiponso woyenera, mulowetseni ufumu wa abambo ake. Kenaka muchite nkhondo kuteteza nyumba ya mbuye wanu.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
musankhe wokoma ndi woyenerayo wa ana a mbuye wanu, ndi kumuika pa mpando wacifumu wa atate wace; ndipo muiponyere nkhondo nyumba ya mbuye wanu.