2 Kings 10:35 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Yehu adamwalira, naikidwa m'manda mu mzinda wa Samariya. Ndipo Yohowahazi mwana wake adaloŵa ufumu ku Israele m'malo mwake.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Nagona Yehu ndi makolo ake, namuika m'Samariya. Ndi Yehowahazi mwana wake anakhala mfumu m'malo mwake.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Yehu anamwalira ndipo anayikidwa mʼmanda pamodzi ndi makolo ake ku Samariya. Ndipo Yehowahazi mwana wake analowa ufumu mʼmalo mwake.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Nagona Yehu ndi makolo ace, namuika m'Samariya. Ndi Yehoahazi mwana wace anakhala mfumu m'malo mwace.