2 Kings 10:4 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma anthuwo adachita mantha kwambiri, ndipo adati, “Ha! Mafumu aŵiri aja sadathe kulimbana naye Yehu, nanga ife ndiye tingathe bwanji?”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma anaopa kwambiri, nati, Taonani, mafumu awiri sanaime pamaso pake, nanga ife tidzaima bwanji?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Koma anthuwo anachita mantha kwambiri ndipo anati, “Taonani, mafumu awiri sanathe kulimbana naye, nanga ife tingathe bwanji?”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma anaopa kwambiri, nati, Taonani, mafumu awiri sanaima pamaso pace, nanga ife tidzaima bwanji?