2 Kings 11:13 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsono mfumukazi Ataliya, atamva phokoso la asilikali ndi la anthu, adapita ku Nyumba ya Chauta.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pamene Ataliya anamva phokoso la otumikira ndi anthu, anadza kwa anthu m'nyumba ya Yehova;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ataliya atamva phokoso limene alonda ndi anthuwo amachita, anapita ku Nyumba ya Yehova kumene kunali anthuwo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pamene Ataliya anamva phokoso la otumikira ndi anthu, anadza kwa anthu m'nyumba ya Yehova;