2 Kings 11:17 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsono Yehoyada adachititsa chipangano pakati pa Chauta ndi mfumu pamodzi ndi anthu ake, kuti iwowo akhale anthu akeake a Chauta. Anthuwo adachitanso chipangano ndi mfumu,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Yehoyada anachita chipangano pakati pa Yehova ndi mfumu ndi anthu, akhale anthu a Yehova; pakati pa mfumunso ndi anthu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Tsono Yehoyada anachititsa pangano pakati pa Yehova ndi mfumu ndi anthu kuti adzakhala anthu a Yehova. Iye anachititsanso pangano pakati pa mfumu ndi anthu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo Yehoyada anacita cipangano pakati pa Yehova ndi mfomu ndi anthu, akhale anthu a Yehova; pakati pa mfumunso ndi anthu.