2 Kings 11:20 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Motero anthu am'dzikomo adakondwa. Ndipo mumzindamo mudakhala bata, Ataliya ataphedwa ku nyumba ya mfumu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Nakondwerera anthu onse a m'dziko, ndi m'mudzi munali phee; ndipo adapha Ataliya ndi lupanga kunyumba ya mfumu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Choncho anthu onse a mʼdzikomo anasangalala. Ndipo mu mzindamo munakhala bata chifukwa Ataliya nʼkuti ataphedwa ndi lupanga ku nyumba ya mfumu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Nakondwerera anthu onse a m'dziko, ndi m'mudzi munali phe; ndipo adapha Ataliya ndi lupanga ku nyumba ya mfumu.