2 Kings 11:21 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Yowasiyo anali wa zaka zisanu ndi ziŵiri pamene adaloŵa ufumu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Yowasi anali wa zaka zisanu ndi ziwiri polowa iye ufumu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Yowasi anali wa zaka zisanu ndi ziwiri pamene anayamba kulamulira.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Yoasi anali wa zaka zisanu ndi ziwiri polowa iye ufumu.