2 Kings 11:3 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mwanayo adakhala ndi mlezi wake zaka zisanu ndi chimodzi akubisala m'Nyumba ya Chauta, pamene Ataliya ankalamulira dzikolo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Nakhala naye wobisika m'nyumba ya Yehova zaka zisanu ndi chimodzi; ndipo Ataliya anakhala mfumu ya dziko.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mwanayo anakhala mobisala pamodzi ndi mlezi wake mʼnyumba ya Yehova kwa zaka zisanu ndi chimodzi pamene Ataliya ankalamulira dzikolo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Nakhala naye wobisika m'nyumba ya Yehova zaka zisanu ndi cimodzi; ndipo Ataliya anakhala mfumu ya dziko.