2 Kings 11:5 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
naŵalamula kuti, “Zimene mudzachite ndi izi: Inu a m'chigaŵo chija choyamba, amene mukudzatumikira pa Sabata, mugaŵikane patatu: gulu limodzi lidzalonde ku nyumba ya mfumu;
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Nawalamulira, kuti, Chochita inu ndi ichi: limodzi la magawo atatu la inu olowa pa Sabata lizilindira nyumba ya mfumu,
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Yehoyada anawalamulira kuti, “Chimene muti muchite ndi ichi: Inu magulu atatu amene muti mudzakhale pa ntchito tsiku la Sabata, gulu loyamba lidzalondera nyumba ya mfumu,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Nawalamulira, kuti, Cocita inu ndi ici: limodzi la magawo atatu la inu olowa pa Sabata lizilindira nyumba ya mfumu,