2 Kings 11:6 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
gulu lachiŵiri lidzalonde pa Chipata cha Suri, gulu lachitatu lidzalonde pa chipata cha kumbuyo kwa asilikali, azilonda pa zipata zoloŵera ku Nyumba ya Chauta.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
ndi lina lizikhala ku chipata cha Suri, ndi lina ku chipata kumbuyo kwa otumikira; momwemo muzisunga nyumba, ndi kuitchinjiriza.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
gulu lachiwiri lidzalondera Chipata cha Suri, ndipo gulu lachitatu lidzalondera chipata cha kumbuyo kwa asilikali amene amasinthana polondera nyumbayo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
ndi lina lizikhala ku cipata ca Suri, ndi lina ku cipata kumbuyo kwa otumikira; momwemo muzisunga nyumba, ndi kuicinjiriza.