2 Kings 12:1 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Chaka chachisanu ndi chiŵiri cha ufumu wa Yehu, Yowasi adaloŵa ufumu ndipo adalamulira zaka makumi anai ku Yerusalemu. Mai wake anali Zibiya wa ku Beereseba.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Chaka chachisanu ndi chiwiri cha Yehu, Yowasi analowa ufumu wake; nakhala mfumu m'Yerusalemu zaka makumi anai; ndi dzina la mai wake ndiye Zibiya wa ku Beereseba.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mʼchaka chachisanu ndi chiwiri cha Yehu, Yowasi anakhala mfumu, ndipo analamulira mu Yerusalemu zaka makumi anayi. Amayi ake anali Zibiya wa ku Beeriseba.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Caka cacisanu ndi ciwiri ca Yehu, Yoasi analowa ufumu wace; nakhala mfumu m'Yerusalemu zaka makumi anai; ndi dzina la mai wace ndiye Zibiya wa ku Beereseba.