2 Kings 12:14 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
pakuti zimenezo ankalipirira antchito okonza Nyumba ya Chauta.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
pakuti anazipereka kwa iwo akugwira ntchitoyi, nakonza nazo nyumba ya Yehova.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndalamazi anazipereka kwa anthu antchito amene anazigwiritsa ntchito yokonzera nyumbayo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
pakuti anazipereka kwa iwo akugwira nchitoyi, nakonza nazo nyumba ya Yehova.