2 Kings 12:20 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Nduna zake zidamchita chiwembu, ndipo zidamupha ku linga la Milo limene lili pa njira yotsikira ku Sila.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo anyamata ake ananyamuka, napangana, nakantha Yowasi kunyumba ya Milo potsikira ku Sila.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Akuluakulu ake anamuchitira chiwembu ndi kumupha ku Beti Milo, pa njira yotsikira ku Silo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo anyamata ace ananyamuka, napangana, nakantha Yoasi ku nyumba ya Milo potsikira ku Silo.