2 Kings 12:3 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Komabe akachisi opembedzerako mafano pa zitunda sadaŵaononge. Anthu adapitirirabe kupereka nsembe ndi kumafukiza lubani pa malo amenewo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma misanje sanaichotse; anthu anapherabe nsembe, nafukiza kumisanje.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Komabe sanachotse malo opembedzerapo mafano ndipo anthu anapitiriza kupereka nsembe ndi kufukiza lubani ku malo opembedzerako mafanowo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma misanje sanaicotsa; anthu anapherabe nsembe, nafukiza komisanje.