2 Kings 12:5 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Wansembe aliyense aziyang'anira ndalama zopereka anthu amene iye amaŵatumikira, ndipo azigwiritse ntchito pokonza Nyumba paliponse pamene pafunika kukonza.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ansembe azilandire yense kwa iye amene adziwana naye, akonze nazo mogamuka nyumba, paliponse akapeza pogamuka.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Wansembe aliyense alandire ndalamazo kuchokera kwa abwenzi ake, ndipo zigwiritsidwe ntchito yokonzera chilichonse chimene chipezeke kuti ndi chowonongeka mʼnyumbayo.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ansembe azilandire yense kwa iye amene adziwana naye, akonze nazo mogamuka nyumba, pali ponse akapeza pogamuka.