2 Kings 12:6 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma pomafika chaka cha 23 cha ufumu wa Yowasi, ansembewo anali asanakonzebe Nyumbayo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma kunali, chaka cha makumi awiri mphambu zitatu cha mfumu Yowasi, ansembe sanathe kukonza mogamuka nyumba.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Koma pofika chaka cha 23 cha ufumu wa Yowasi, ansembewo anali asanakonze nyumbayo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma kunali, caka ca makumi awiri mphambu zitatu ca Yoasi sanathe kukonza mogamuka nyumba.