2 Kings 12:8 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Motero ansembe aja adavomera kuti sadzatenganso ndalama kwa anthu, ndipo kuti sindiwo adzakonza Nyumbayo, koma ena.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Navomera ansembe kusalandiranso ndalama za anthu, kapena kukonza mogamuka nyumba.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ansembe anavomera kuti salandiranso ndalama kuchokera kwa anthu ndipo kuti sindiwo amene ati akonzenso nyumbayo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Nabvomera ansembe kusalandiranso ndarama za anthu, kapena kukonza mogamuka nvumba.