2 Kings 13:10 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Chaka cha 37 cha ufumu wa Yowasi mfumu ya ku Yuda, Yehowasi mwana wa Yehowahazi adayamba kulamulira Aisraele ku Samariya, ndipo adalamulira zaka 16.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Chaka cha makumi atatu ndi zisanu ndi ziwiri cha Yowasi mfumu ya Yuda, Yehowasi mwana wa Yehowahazi analowa ufumu wake wa Israele m'Samariya, nakhala mfumu zaka khumi ndi zisanu ndi chimodzi.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mʼchaka cha 37 cha Yowasi mfumu ya Yuda, Yehowahazi anakhala mfumu ya Israeli mu Samariya, ndipo analamulira zaka 16.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Caka ca makumi atatu ndi zisanu ndi ziwiri ca Yoasi mfumu ya Yuda, Yoasi mwana wa Yoahazi analowa ufumu wace wa Israyeli m'Samariya, nakhala mfumu zaka khumi ndi zisanu ndi cimodzi.