2 Kings 13:24 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Hazaele mfumu ya ku Siriya atamwalira, Benihadadi mwana wake adaloŵa ufumu m'malo mwake.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Nafa Hazaele mfumu ya Aramu, nakhala mfumu m'malo mwake Benihadadi mwana wake.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Hazaeli mfumu ya Aramu inamwalira ndipo mwana wake Beni-Hadadi analowa ufumu mʼmalo mwake.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Nafa Hazaeli mfumu ya Aramu, nakhala mfumu m'malo mwace Benihadadi mwana wace.