2 Kings 13:5 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Nchifukwa chake Chauta adasankha mtsogoleri kuti apulumutse Aisraele m'manja mwa Asiriya. Motero Aisraele adakhala mwamtendere m'dziko mwao, monga momwe ankakhalira kale.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Yehova anapatsa Israele mpulumutsi, natuluka iwo pansi pa dzanja la Aaramu; nakhala ana a Israele m'mahema mwao monga kale.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Yehova anapatsa Aisraeli munthu woti awapulumutse ndipo anapulumuka mʼdzanja la Aramu. Choncho Aisraeli anakhala mʼnyumba zawo monga ankachitira kale.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo Yehova anapatsa Israyeli mpulumutsi, naturuka iwo pansi pa dzanja la Aaramu; nakhala ana a Israyeli m'mahema mwao monga kale.