2 Kings 13:9 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Motero Yehowahazi adamwalira, naikidwa m'manda momwe adaikidwa makolo akewo ku Samariya. Tsono Yehowasi mwana wake adaloŵa ufumu m'malo mwake.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Yehowahazi anagona ndi makolo ake, namuika m'Samariya; nakhala mfumu m'malo mwake Yowasi mwana wake.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Yehowahazi anamwalira ndipo anayikidwa mʼmanda mu Samariya. Ndipo Yowasi mwana wake analowa ufumu mʼmalo mwake.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo Yoahazi anagona ndi makolo ace, namuika m'Samariya; nakhala mfumu m'malo mwace Yoasi mwana wace.