2 Kings 14:17 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Amaziya mwana wa Yowasi, mfumu ya ku Yuda, adakhala moyo zaka 15 atafa Yehowasi, mwana wa Yehowahazi, mfumu ya ku Israele.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Amaziya mwana wa Yowasi mfumu ya Yuda anakhala ndi moyo, atamwalira Yehowasi mwana wa Yehowahazi mfumu ya Israele, zaka khumi ndi zisanu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Amaziya mwana wa Yowasi mfumu ya Yuda anakhala zaka khumi ndi zisanu atamwalira Yehowasi mwana wa Yehowahazi mfumu ya Israeli.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo Amaziya mwana wa Yoasi mfumu ya Yuda anakhala ndi moyo, atamwalira Yoasi mwana wa Yoahazi mfumu ya Israyeli, zaka khumi ndi zisanu.