2 Kings 14:18 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsono ntchito zina zonse zimene adachita Amaziya zidalembedwa m'buku la Mbiri ya Mafumu a ku Yuda.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Machitidwe ena tsono a Amaziya, sanalembedwa kodi m'buku la machitidwe a mafumu a Yuda?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ntchito zina za Amaziya, kodi sizinalembedwe mʼbuku la mbiri ya mafumu a Yuda?
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Macitidwe ena tsono a Amaziya, kodi sizilembedwa m'buku la macitidwe a mafumu a Yuda?