2 Kings 14:26 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Chauta adaona kuti mavuto a Aisraele anali oopsa. Panalibe ndi mmodzi yemwe wotsala, kapolo kapena mfulu, woti angaŵathandize Aisraelewo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pakuti Yehova anapenya kuti kuzunzika kwao kwa Israele nkowawa ndithu; popeza panalibe womangika kapena womasuka, ndipo panalibe womthandiza Israele.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pakuti Yehova anaona masautso a Israeli amene anali owawa kwambiri, panalibe kapolo kapena mfulu ngakhale wina aliyense amene akanathandiza Israeli.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pakuti Yehova anapenya kuti kuzunzika kwao kwa Israyeli nkowawa ndithu; popeza panalibe womangika kapena womasuka, ndipo panalibe womthandiza Israyeli.