2 Kings 14:5 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Atangolandira mphamvu zonse zaufumu m'manja mwake, Amaziya adapha anyamata ake amene adaapha mfumu ija, bambo wake. Koma ana a anthuwo sadaŵaphe,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo kunali, utakhazikika ufumu m'dzanja lake, anakantha anyamata ake amene adakantha mfumu atate wake;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Atakhazikika mu ufumu wake, Amaziya anapha atumiki ake amene anapha abambo ake, mfumu ija.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo kunali, utakhazikika ufumu m'dzanja lace, anakantha anyamata ace amene adakantha mfumu atate wace;