2 Kings 14:8 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Nthaŵi ina Amaziya adatuma amithenga kwa Yehowasi mwana wa Yehowahazi, mdzukulu wa Yehu, mfumu ya ku Israele, kukanena momputa kuti, “Ubwere kuno, tidzaonane maso ndi maso.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pamenepo Amaziya anatuma mithenga kwa Yehowasi mwana wa Yehowahazi mwana wa Yehu mfumu ya Israele, ndi kuti, Idzani tionane maso.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Tsono Amaziya anatuma amithenga kwa Yehowasi mwana wa Yehowahazi, mwana wa Yehu mfumu ya Israeli ndi kumuopseza kuti, “Bwera tidzaonane maso ndi maso.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pamenepo Amaziya anatuma mithenga kwa Yoasi mwana wa Yoahazi mwana wa Yehu mfumu ya Israyeli, ndi kuti, Idzani tionane maso.