2 Kings 15:1 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Chaka cha 27 cha ufumu wa Yerobowamu mfumu ya ku Israele, Azariya mwana wa Amaziya mfumu ya ku Yuda, adaloŵa ufumu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Chaka cha makumi awiri mphambu zisanu ndi ziwiri cha Yerobowamu mfumu ya Israele, Azariya mwana wa Amaziya mfumu ya Yuda analowa ufumu wake.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mʼchaka cha 27 cha Yeroboamu mfumu ya Israeli, Azariya mwana wa Amaziya mfumu ya Yuda anayamba kulamulira.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Caka ca makumi awiri mphambu zisanu ndi ziwiri ca Yerobiamu mfumu ya Israyeli, Azariya mwana wa Amaziya mfumu ya Yuda analowa ufumu wace.