2 Kings 15:2 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Iyeyu anali wa zaka 16 pamene adaloŵa ufumu, ndipo adalamulira zaka 52 ku Yerusalemu. Mai wake anali Yekoliya wa ku Yerusalemu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Anali wa zaka khumi ndi zisanu ndi chimodzi polowa ufumu wake, nakhala mfumu zaka makumi asanu mphambu ziwiri m'Yerusalemu; ndi dzina la make ndiye Yekoliya wa ku Yerusalemu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iye anakhala mfumu ali ndi zaka 16 ndipo analamulira mu Yerusalemu zaka 52. Amayi ake anali Yekoliya wa ku Yerusalemu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Anali wa zaka khumi ndi zisanu ndi cimodzi polowa ufumu wace, nakhala mfumu zaka makumi asanu mphambu ziwiri m'Yerusalemu; ndi dzina la mace ndiye Yekoliya wa ku Yerusalemu.