2 Kings 15:22 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndipo Menahemu adamwalira, naikidwa m'manda momwe adaikidwa makolo akewo. Tsono Pekahiya mwana wake adaloŵa ufumu m'malo mwake.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Nagona Menahemu ndi makolo ake; nakhala mfumu m'malo mwake Pekahiya mwana wake.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Menahemu anamwalira ndipo anayikidwa mʼmanda pamodzi ndi makolo ake. Ndipo Pekahiya mwana wake analowa ufumu mʼmalo mwake.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Nagona Menahemu ndi makolo ace; nakhala mfumu m'malo mwace Pekahiya mwana wace.