2 Kings 15:32 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Chaka chachiŵiri cha ufumu wa Peka mwana wa Remaliya, mfumu ya ku Israele, Yotamu mwana wa Uziya mfumu ya ku Yuda, adaloŵa ufumu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Chaka chachiwiri cha Peka mwana wa Remaliya mfumu ya Israele, Yotamu mwana wa Uziya mfumu ya Yuda analowa ufumu wake.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mʼchaka chachiwiri cha Peka mwana wa Remaliya mfumu ya Israeli, Yotamu mwana wa Uziya mfumu ya Yuda anayamba kulamulira.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Caka caciwiri ca Peka mwana wa Remaliya mfumu ya Israyeli, Yotamu mwana wa Uziya mfumu ya Yuda analowa ufumu wace.