2 Kings 15:7 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndipo adamwalira naikidwa m'manda momwe adaikidwa makolo akewo mu mzinda wa Davide. Ndiye Yotamu mwana wake adaloŵa ufumu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Nagona Azariya ndi makolo ake, namuika ndi makolo ake m'mudzi wa Davide; nakhala mfumu m'malo mwake Yotamu mwana wake.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Azariya anamwalira ndipo anayikidwa mʼmanda pamodzi ndi makolo ake mu Mzinda wa Davide. Ndipo Yotamu mwana wake analowa ufumu mʼmalo mwake.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Nagona Azariya ndi makolo ace, namuika ndi makolo ace m'mudzi wa Davide; nakhala mfumu m'malo mwace Yotamu mwana wace.