2 Kings 16:1 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Chaka cha 17 cha ufumu wa Peka mwana wa Remaliya, Ahazi mwana wa Yotamu mfumu ya ku Yuda, adaloŵa ufumu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Chaka chakhumi mphambu zisanu ndi ziwiri cha Peka mwana wa Remaliya Ahazi mwana wa Yotamu mfumu ya Yuda analowa ufumu wake.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mʼchaka cha 17 cha Peka mwana wa Remaliya, Ahazi mwana wa Yotamu mfumu ya Yuda anayamba kulamulira.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Caka cakhumi mphambu zisanu ndi ziwiri ca Peka mwana wa Remaliya Ahazi mwana wa Yotamu mfumu ya Yuda analowa ufumu wace.