2 Kings 16:12 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mfumu itabwera kuchokera ku Damasiko, nipenya guwa lija, idasendera pafupi ndi guwalo ndi kukwera kuguwako.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Atafika mfumu kuchokera ku Damasiko, anapenya mfumu guwa la nsembelo, nayandikiza mfumu ku guwa la nsembelo, napereka nsembe pomwepo.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mfumu itabwera kuchokera ku Damasiko kuja ndi kuona guwalo, inasendera pafupi ndi kupereka nsembe paguwapo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Atafika mfumu kucokera ku Damasiko, anapenya mfumu guwa la nsembelo, nayandikiza mfumu ku guwa la nsembelo, napereka nsembe pomwepo.