2 Kings 17:14 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma anthuwo sankamva, anali ouma mitu monga momwe analiri makolo ao amene sadakhulupirire Chauta Mulungu wao.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma sanamvere, naumitsa khosi lao, monga khosi la makolo ao amene sanakhulupirire Yehova Mulungu wao.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Koma anthuwa sanamvere ndipo anawumitsa khosi ngati momwe analili makolo awo, amene sanadalire Yehova Mulungu wawo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma sanamvera, naumitsa khosi lao, monga khosi la makolo ao amene sanakhulupirira Yehova Mulungu wao.