2 Kings 17:19 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Nawonso a fuko la Yuda sadasunge malamulo a Chauta Mulungu wao, koma ankayenda motsata miyambo imene Aisraele adaiyambitsa.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Yudanso sanasunge malamulo a Yehova Mulungu wao, koma anayenda m'malemba a Israele amene adawaika.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Yuda nayenso sanasunge malamulo a Yehova Mulungu wawo. Iwo ankatsatira machitidwe amene Israeli anayambitsa.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Yudansosanasunga malamulo a Yehova Mulungu wao, koma anayenda m'malemba a Israyeli amene adawaika.