2 Kings 17:20 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Choncho Chauta adakana zidzukulu zonse za Aisraele, nazizunza, nkuzipereka mu ulamuliro wa anthu ofunkha, mpaka ataŵachotseratu onse.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Yehova anakaniza mbumba yonse ya Israele, nawazunza, nawapereka m'dzanja la ofunkha, mpaka anawataya pamaso pake.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Motero Yehova anakana Aisraeli onse. Iye anawazunza nawapereka mʼmanja mwa anthu ofunkha mpaka Iye atawachotseratu pamaso pake.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo Yehova anakaniza mbumba yonse ya Israyeli, nawazunza, nawapereka m'dzanja la ofunkha, mpaka anawataya pamaso pace.