2 Kings 17:25 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma iwowo chiloŵere chao kumeneko sankapembedza Chauta. Nchifukwa chake Chauta adatumiza mikango pakati pao, nipha ena mwa iwowo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo kunali, poyamba iwo kukhala komweko, sanaope Yehova; ndipo Yehova anawatumizira mikango, niwapha ena a iwowa.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iwo atayamba kukhala kumeneko, sanapembedze Yehova choncho Yehova anatumiza mikango pakati pawo ndipo inapha ena mwa iwo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo kunali, poyamba iwo kukhala komweko, sanaopa Yehova; ndipo Yehova anawatumizira mikango, niwapha ena a iwowa.