2 Kings 17:27 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsono mfumu ya ku Aasiriya idalamula kuti, “Tumani mmodzi mwa ansembe amene mudaŵagwira kumeneko, akakhale komweko, kuti akaŵaphunzitse kupembedza Mulungu wa dzikolo.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pamenepo mfumu ya Asiriya analamulira, kuti, Mukani naye komweko wina wa ansembe munawachotsako, nakakhale komweko, akawalangize makhalidwe a Mulungu wa dzikoli.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Tsono mfumu ya ku Asiriya inalamula kuti, “Tengani wansembe mmodzi mwa amene munawagwira ukapolo, mupite naye kumeneko ndipo akakhale komweko nakaphunzitse anthu zimene Mulungu wa dzikolo amafuna.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pamenepo mfumu ya Asuri analamulira, kuti, Mukani naye komweko wina wa ansembe munawacotsako, nakakhale komweko, akawalangize makhalidwe a Mulungu wa dzikoli.