2 Kings 17:30 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Anthu a ku Babiloni adadzipangira fano lotchedwa Sukoti-Benoti. Anthu a ku Kuta adapanga fano lotchedwa Neregali, anthu a ku Hamati adapanga fano lotchedwa Ashima.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo anthu a Babiloni anapanga Sukoti-Benoti, ndi anthu a Kuta anapanga Neregali, ndi anthu a Hamati anapanga Ashima,
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Anthu a ku Babuloni anapanga Sukoti-Benoti, anthu a ku Kuti anapanga Nerigali, ndipo anthu a ku Hamati anapanga Asima;
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo anthu a Babulo anapanga Sukoti Bemoti, ndi anthu a Kuta anapanga Nerigali, ndi anthu a Hamati anapanga Asima,