2 Kings 17:31 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Aavi adapanga fano lotchedwa Nibihazi ndiponso Taritaki. Asefaravaimu ankapereka ana ao ngati nsembe zopsereza kwa Adrameleki ndi kwa Anameleki, milungu ya Asefaravaimu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
ndi Aavi anapanga Nibihazi ndi Taritaki; ndi a Sefaravaimu anawatentha ana ao m'moto kwa Adrameleki, ndi Anameleki, milungu ya Asefaravaimu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Aava anapanga Nibihazi ndi Taritaki, ndipo Asefaravaimu ankawotcha ana awo pa moto ngati nsembe kwa Adirameleki ndi Anameleki, milungu ya Asefaravaimu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
ndi Aava anapanga Nibazi ndi Tarataka; ndi a Sefaravaimu anawatentha ana ao m'moto kwa Adrameleki, ndi Anameleki, milungu ya Asefaravaimu.