2 Kings 17:33 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Motero ankapembedza Chauta, kwinaku ankatumikirabe milungu yao, potsata makhalidwe a mitundu ya anthu a kumene adatengedwa ukapoloko.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Amaopa Yehova, namatumikiranso milungu yao, monga mwa miyambo ya amitundu anawachotsako.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iwowo ankapembedza Yehova, komanso ankatumikira milungu yawo molingana ndi miyambo ya mitundu ya kumene ankachokera.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Amaopa Yehova, namatumikiranso milungu yao, monga mwa miyambo ya amitundu anawacotsako.