2 Kings 17:35 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Chauta adaachita nawo Aisraele chipangano naŵalamula kuti, “Musapembedze milungu ina kapena kuilambira kapena kuitumikira, kapena kuiperekera nsembe.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
ndiwo amene Yehova adapangana nao, nawalamulira, ndi kuti, Musamaopa milungu ina, kapena kuigwadira, kapena kuitumikira, kapena kuiphera nsembe;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pamene Yehova anachita pangano ndi Aisraeli, Iye anawalamula kuti, “Musapembedze milungu ina kapena kuyigwadira iyo, kuyitumikira kapena kupereka nsembe kwa iyoyo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
ndiwo amene Yehova adapangana nao, nawalamulira, ndi kuti, Musamaopa milungu yina, kapena kuigwadira, kapena kuitumikira, kapena kuiphera nsembe;