2 Kings 17:40 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Komabe iwowo sankamva zimenezi, koma ankachitabe zimene adakhala akuchita kuyambira kale.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma sanamvere, nachita monga mwa mwambo wao woyamba.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Komabe iwo sanamvere ndipo anapitiriza kuchita zomwe ankachita kale.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma sanamvera, nacita monga mwa mwambo wao woyamba.