2 Kings 18:1 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Chaka chachitatu cha ufumu wa Hoseya, mwana wa Ela, mfumu ya ku Israele, Hezekiya, mwana wa Ahazi, mfumu ya ku Yuda, adaloŵa ufumu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo kunali chaka chachitatu cha Hoseya mwana wa Ela mfumu ya Israele, Hezekiya mwana wa Ahazi mfumu ya Yuda analowa ufumu wake.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mʼchaka chachitatu cha Hoseya mwana wa Ela mfumu ya Israeli, Hezekiya mwana wa Ahazi mfumu ya Yuda analowa ufumu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo kunali caka cacitatu ca Hoseya mwana wa Ela mfumu ya Israyeli, Hezekiya mwana wa Ahazi mfumu ya Yuda analowa ufumu waceo