2 Kings 18:13 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Chaka cha 14 cha ufumu wa Hezekiya, Senakeribu mfumu ya ku Asiriya adadzathira nkhondo mizinda yonse yamalinga ya ku Yuda nailanda.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Chaka chakhumi ndi zinai cha Hezekiya Senakeribu mfumu ya Asiriya anakwerera midzi yonse ya malinga ya Yuda, nailanda.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mʼchaka chakhumi ndi chinayi cha ulamuliro wa Mfumu Hezekiya, Senakeribu mfumu ya ku Asiriya anathira nkhondo mizinda yonse yotetezedwa ya Yuda, nayilanda.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Caka cakhumi ndi zinai ca Hezekiya Sanakeribu mfumu ya Asuri anakwerera midzi yonse ya malinga ya Yuda, nailanda.