2 Kings 18:19 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Kazembe wankhondo uja adaŵauza kuti akanene kwa Hezekiya mau aŵa: “Mfumu yaikulu, mfumu ya ku Asiriya, ikuti, ‘Chimene chikulimbitsa chikhulupiriro chako motere nchiyani?
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Nanena nao kazembeyo, Muuzetu Hezekiya, Itero mfumu yaikulu, mfumu ya Asiriya, Chikhulupiriro ichi nchotani uchikhulupirira?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndipo Rabusake anawawuza kuti, “Kamuwuzeni Hezekiya kuti, “ ‘Mfumu yayikulu, mfumu ya ku Asiriya ikunena kuti, ‘Kodi chikukulimbitsa mtima ndi chiyani?’
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Nanena nao kazembeyo, Muuzetu Hezekiya, Itero mfumu yaikuru, mfumu ya Asuri, Cikhulupiriro ici ncotani ucikhulupirira?