2 Kings 18:29 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mfumuyo ikuti, Musalole kuti Hezekiya akunyengeni, chifukwa sadzatha kukupulumutsani m'manja mwanga.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Itero mfumu, Asakunyengeni Hezekiya; pakuti sadzakhoza kukulanditsani m'dzanja lake;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Zimene mfumu ikunena ndi izi: ‘Musalole kuti Hezekiya akunamizeni. Iye sangakupulumutseni mʼdzanja langa.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Itero mfumu, Asakunyengeni Hezekiya; pakuti sadzakhoza kukulanditsani m'dzanja lace;